nya-x-nyanja_2jn_text_reg/01/07.txt

1 line
249 B
Plaintext

\v 7 Pakuti bambiri babodza bapita muziko lapansi, ndipo sibazindikila kuti Yesus Kristu anabwela mu tupi. Uyo ndiye wabodza wosusha Kristu. \v 8 Wonesesani pakati panu , kuti musateye zinthu zamene tasebenzela, koma kuti mukalandile mphaso yokwana.