Fri Nov 09 2018 17:03:48 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2018-11-09 17:03:49 +02:00
parent 5213c918ff
commit da38dfda8e
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\c 1 \v 1 Kucokela ku mukulu wamupingo mukazi wosankhiwa ndibana bake, wamene nikonda muchonadi- \v 2 ndipo sindine neka,chifukwa cha choonadi chamene chinasala mwaise ndipo choonadi chizakhalila mwaise muyayaya. \v 3 Lekani chisomo,chifundo na mtendere zinkale naise kucokela kuli mulungu tate nakuli Yesu Kristu,mwana wa atate,muchoonadi namu chikondi.
\c 1 \v 1 Kucokela ku mukulu wamupingo kwa mukazi wosankhiwa na bana bake, wamene nikonda muchonadi- \v 2 ndipo sindine neka chifukwa cha choonadi chamene chinasala mwaise ndipo choonadi chizankhalila mwaise muyayaya. \v 3 Lekani chisomo, chifundo na mutendere zinkale naise kucokela kuli Mulungu Atate nakuli Yesu Kristu,mwana wa atate,muchoonadi namu chikondi.