Fri Nov 09 2018 17:07:48 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2018-11-09 17:07:49 +02:00
parent 790b79fb03
commit 5d787112da
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 4 Nakondwela maningi kupeza bana banu bena bayenda muchoonadi, monga mwamene tinalandilila malamulo kuchokela kuli Mulungu. \v 5 Apa namupapatilani, mukazi - osati monga nilemba malamulo yasopano,koma amodzi tilinaye kuchiyambi-kuti tizikondana. \v 6 Ndiponso ichi ndi chikondi,ndiye icho tiyende mukulingana namalamulo. Aya ndiye malamulo,monga mwamene munavelela kuchiyambi,ndipo yenda muli ichi.
\v 4 Nakondwela maningi kupeza bana banu bena bayenda muchoonadi, monga mwamene tinalandilila malamulo kuchokela kuli Mulungu. \v 5 Apa namupapatilani, mukazi - osati monga nilemba malamulo yasopano, koma amozi tilinaye kuchiyambi - kuti tizikondana. \v 6 Ndiponso ichi ndi chikondi, kuti tiziyenda mukulingana namalamulo. Aya ndiye malamulo,monga mwamene munavelela kuchiyambi,ndipo yenda muli ichi.