nya-x-nyanja_1pe_text_reg/04/15.txt

1 line
209 B
Plaintext

\v 15 Koma musa vutike chifukwa chakuti munapaya, kawalala, kuchita zonyansa, ongenela za bene. \v 16 Koma kapena wina avutika kamba ka Yesu, lekani asannvele nsoni. Koma siyani alemekeze Mulungu na zina ija.