nya-x-nyanja_1pe_text_reg/03/08.txt

1 line
246 B
Plaintext

\v 8 Naposiliza, imwe monse,nkalani ba maganizo yamozi, ba chifundo bokondana, ba mitima yabwino. \v 9 Osabwezela choipa pa choipa naku tukwana paku tukwana, osa chita izo pitilizani ku dalisa chifukwa chaichi muna itanidwa, kuti mutenge daliso.