nya-x-nyanja_1pe_text_reg/02/11.txt

1 line
279 B
Plaintext

\v 11 okondeka,nikuitanani monga balendo nabo endaenda osiya zaku mubili,zamene zima chita ndeo na moyo wanu. \v 12 Muyenela ku chita bwino pamene muli paosaniziba,kuti,kapena bakamba kuti munachita vintu zoipa,kutibaone nchitozanu zabwino kuti bayamike mulungu pakubwela kwake.