nya-x-nyanja_1jn_text_reg/05/01.txt

1 line
348 B
Plaintext

\c 5 \v 1 \v 2 \v 3 Alionse wamene akhulupilila kuti yesu ni mfumu anabadwa kwa Mulungu, ndiponso wamene akonda tate ndiponso akonda mwana wamene anabadwa kwaiye. chifukwa chaichi tiziba kuti tikonda bana bamulungu: ngati takonda ndi kuchita malamulo yamulungu. ichi ndiye chikondi chamulungu: kuti tisunge malamulo yake. ndimalamulo yake siyolema.