nya-x-nyanja_1jn_text_reg/05/20.txt

1 line
255 B
Plaintext

\v 20 Koma tiziba kuti mwana wamulungu anabwela, ndiponso anatipasa kumvesesa uyo wamene ilina choonadi.koma, tilinaye wamene alina choonadi, mu mwana wake Yesu kristhu.Mulungu ndiye choonadi ndi moyo wamuyayaya. \v 21 Imwe bana, zichosenikoni kumafano.