nya-x-nyanja_1jn_text_reg/05/18.txt

1 line
266 B
Plaintext

\v 18 Tiziba kuti onse wamene anabadwa kwa Mulungu siamachimwa. koma uyo wamene anabadwa kuchokela kwa Mulungu amamusunga bwino kwaiyo eka, ndiponso uja woipa sianga muononge. \v 19 Tiziba kuti tichokela kwa Mulungu, ndiponso tiziba kuti ziko lonse zinkala muzoipa.