nya-x-nyanja_1jn_text_reg/05/13.txt

1 line
387 B
Plaintext

\v 13 Nilembela izi zinthu kuti, kuti muzibe kuti mulina umoyo wamuyayaya__kuli imwe bamene bakulupilila mu zina la mwana wa Mulungu. \v 14 Ndiponso ichi ndiye chizindikilo chamene tili nacho mwa iye, kuti tikamufunsa chilichonse kulinganila na chifuniro chake, ama timvela. \v 15 Ndiponso, ngati amatimvela ise_ chilichonse chamene tizamufunsa_tiziba kuti tapasidwa chamene tamufunsa.