nya-x-nyanja_1jn_text_reg/04/11.txt

1 line
395 B
Plaintext

\v 11 Bokondedwa,ngati mulungu anatikonda,naise tikondane. \v 12 Kulibe anaonapo mulungu. Ngati tikondana mulungu ankala muli ise. Nachikondi chake nichosilizika muli ise. \v 13 Pali ichi tiziba ati tinkalilila muli iye na iye muli ise,chifukwa anatipasako mbali mbali yamuzimu wake. \v 14 Ndiponso,tinaona ndikupelekela umboni kuti mulungu anatuma mwana wake kubwela kunkala mupulumusi wa ziko.