nya-x-nyanja_1jn_text_reg/04/09.txt

1 line
273 B
Plaintext

\v 9 Cifukwa chaichi chikondi cha mulungu chinavumbulisiwa pali ise,kuti mulungu anatuma mwana wake eka muziko pakuti tinkale cifukwa cha iye. \v 10 Umu mu chikondi,sikuti tinamukonda mulungu,koma anatikonda,ndiponso anatuma mwana wake kunkala otikambilako kuma chimo watu.