nya-x-nyanja_1jn_text_reg/03/19.txt

1 line
420 B
Plaintext

\v 19 Ndi mwaici mwamene tiziba kuti tinachokela kuchoonadi, ndipo tisimikiza mitima yasu pamenso pake. \v 20 Ngati mitima yathu itisusa, Mulungu nimukulu kupambana mitima yathu, Ndipo aziba zithu zonse. \v 21 Wokondedwa, ngati mitima yathu siitisusa, tili ndi chisimikizo kwa Mulungu. \v 22 Chilichonse camene timpempa tiza landila kuchokela kwa iye, chifukwa tisunga malamulo ndipo tichita zamene zimukondwelesa iye.