nya-x-nyanja_1jn_text_reg/03/16.txt

1 line
404 B
Plaintext

\v 16 Mwaichi tiziba chikondi, chifukwa Kristu anataya moyo wake chifukwa ca ise.naise tifunika kutaya moyo wake chifukwa cha abale athu. \v 17 koma aliyese ali na kathundu wamuziko, naona mbale wake akufuna nakuvala mutima wake wachifundo kwayeve, Nanga chikondi cha Mulungu chinkhala bwaji mwa iye? \v 18 Bana banga okondedwa, tisakonde ndi mau cabe kapena ndililime cabe, koma mukucita ndi mchoonadi.