nya-x-nyanja_1jn_text_reg/03/09.txt

1 line
310 B
Plaintext

\v 9 Aliwonse anabadwa mwa Mulungu samachimwa chifukwa mbeu ya Mulungu inkhalilila mwa iye Sangapitilize kuchimwa chifukwa anabadwa kufumila mwa Mulungu. \v 10 Mwaichi bana ba Mulungu ndi ana ba satana ba onekela. Aliyense wamene sachita chilungamo sachokela kwa Mulungu, ngakale iye amene sakonde mbale wake.