nya-x-nyanja_1jn_text_reg/03/07.txt

1 line
273 B
Plaintext

\v 7 Bana anga okondedwa, musalole aliwose akusobeseni. wamene achita chilungamo niolungama. \v 8 Monga Kristu niolungama.Amene acita cimo ni wasatana, Chifukwa satana anacimwa kuchoka pachiyambi. Pa chifukwa ici mwana wa Mulungu anaonesedwa, kuti aononge nchito ya satana