nya-x-nyanja_1jn_text_reg/03/04.txt

1 line
287 B
Plaintext

\v 4 Aliwonse wamene apitiliza kucimwa achita vosa vomelekezedwa, cimo nicosa vomelekezedwa. \v 5 Muziba kuti Kristu anaonesedwa kuti achose cimo. Ndipo mwa iye mulibe cimo. \v 6 Kulibe amene akhala mwa iye apitiliza kucimwa, kulibe amene apitiliza kuchimwa anamuona kapena kumuziba iye.