nya-x-nyanja_1jn_text_reg/02/18.txt

1 line
332 B
Plaintext

\v 18 Imwe bana bango'no, iyi ni ntawi yosilizila, monga mwamene munamvelela kuti bambili bosusana kristhu babwela.paichi tiziba kuti ni ntawi yosilizila. \v 19 Banachokela kuliise , koma sibana chokele mwaise. chifukwa ngati banalikuchokela mwaise, asembe anankhalilila mwaise. koma pamene banaenda, sibalangiza kuchokela kuliise.