nya-x-nyanja_1jn_text_reg/02/12.txt

1 line
437 B
Plaintext

\v 12 Nilembela imwe, bana, chifukwa machimo yanu yakululukidwa chifukwa chazina yake. Nilembela kwainu azitate, chifukwa muziba wamene ili kuchiyambi. \v 13 Nilembela inu amuna achichepele, chifukwa muna gonjesa woyipa. \v 14 Nalembela kwainu atate, chifukwa mumuziba uja wamene anali kuchiyambi. Nalembela kwainu amuna achichepele, chifukwa ndimwe olimba, ndipo mau ya Mulungu yankalilila mwa imwe. ndiponso mwagonjesa uja woyipa.