nya-x-nyanja_1jn_text_reg/02/07.txt

1 line
296 B
Plaintext

\v 7 Okondedwa, sinikulembela malamulo ya sopano kuli iwe, koma niya kudala yamene munali nayo pachiyambi. malamulo yakudala ndiye mau unamvela. \v 8 komanso ni kulembela malamulo yasopano kuli iwe, ndiye ya choonadi muli kristhu, chifukwa mfinzi ilikupita, ndi nyali yachendi ilikuwala kudala.