nya-x-nyanja_1jn_text_reg/01/05.txt

1 line
366 B
Plaintext

\v 5 Uyu ndiye uthenga wamene tinamva, kucokela kwa iye ndi kulalikidwa kwa inu: Mulungu ndiye kuunika, ndipo mwayeve mulibiletu mudima. \v 6 Ngati tikamba kuti tili mucigwilizano ndi iye ndipo tuyenda mumudima, tikamba bodza ndipo siticita choonadi. \v 7 Koma ngati tiyenda mukuunika mwamene iye ali kuunika, ndipo mulopa wa Yesu Mwana wake utisukha kumachimo athu.