nya-x-nyanja_1jn_text_reg/01/03.txt

1 line
238 B
Plaintext

\v 3 Chija camene tinaona ndi kumva ticilankhulanso kwa inu, kuti munkhalenso ndi chiyanjano ndi ife. Chiyanjano cathu cili ndi Atate ndi Mwana, Yesu Kristu. \v 4 Futi tilemba vinthu ivi kuli imwe kuti chimwemwe cathu cinkhale cokwanila.