\v 11 Uyu ndiye uthenga wamene munavela kufumila pachiyambi: kuti tizikondana wina ndi muzake, \v 12 osati monga Kaini, amene anacoka kuwoyipa napaya mubale wake. Nanga anamu paila chani? chifukwa nchito zake zinali zoyipa, ndipo mbale wake zinali zachilungamo.