diff --git a/05/16.txt b/05/16.txt index 368a40f..2560343 100644 --- a/05/16.txt +++ b/05/16.txt @@ -1 +1 @@ -\v 16 \v 17 Ngati alionse aona mubale wake achita chimo yamene siipeleka kuimfa, afunika apempele, ndi Mulungu azamupasa umoyo. nimayanganilako kuli abo bamene machimo yao siapeleka kuimfa. kuli chimo yamene isanduka ku imfa; sinikamba kuti anga pempele pali icho. Zonse zamene siziliza ulungamo ni imfa, koma kuli chimo yamene siisandukala ku imfa. \ No newline at end of file +\v 16 Ngati alionse aona mubale wake achita chimo yamene siipeleka kuimfa, afunika apempele, ndi Mulungu azamupasa umoyo. nimayanganilako kuli abo bamene machimo yao siapeleka kuimfa. kuli chimo yamene isanduka ku imfa; sinikamba kuti anga pempele pali icho. \v 17 Zonse zamene siziliza ulungamo ni chimo, koma kuli chimo yamene siisandukala ku imfa. \ No newline at end of file diff --git a/05/18.txt b/05/18.txt index 18e826e..2e67616 100644 --- a/05/18.txt +++ b/05/18.txt @@ -1 +1 @@ -\v 18 \v 19 Tiziba kuti onse wamene anabadwa kwa Mulungu siamachimwa. koma uyo wamene anabadwa kuchokela kwa Mulungu amamusunga bwino kwaiyo eka, ndiponso uja woipa sianga muononge. Tiziba kuti tichokela kwa Mulungu, ndiponso tiziba kuti ziko lonse zinkala muzoipa. \ No newline at end of file +\v 18 Tiziba kuti onse wamene anabadwa kwa Mulungu siamachimwa. koma uyo wamene anabadwa kuchokela kwa Mulungu amamusunga bwino kwaiyo eka, ndiponso uja woipa sianga muononge. \v 19 Tiziba kuti tichokela kwa Mulungu, ndiponso tiziba kuti ziko lonse zinkala muzoipa. \ No newline at end of file