Fri Nov 09 2018 18:19:53 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2018-11-09 18:19:53 +02:00
parent b3de32dfb9
commit 5fbc6bfc69
2 changed files with 2 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 16 \v 17 \v 18 Mwaichi tiziba chikondi, chifukwa Kristu anataya moyo wake chifukwa ca ise.naise tifunika kutaya moyo wake chifukwa cha abale athu. koma aliyese ali na kathundu wamuziko, naona mbale wake akufuna nakuvala mutima wake wachifundo kwayeve, Nanga chikondi cha Mulungu chinkhala bwaji mwa iye? Bana banga okondedwa, tisakonde ndi mau cabe kapena ndililime koma mukuchita na choonadi.
\v 16 Mwaichi tiziba chikondi, chifukwa Kristu anataya moyo wake chifukwa ca ise.naise tifunika kutaya moyo wake chifukwa cha abale athu. \v 17 koma aliyese ali na kathundu wamuziko, naona mbale wake akufuna nakuvala mutima wake wachifundo kwayeve, Nanga chikondi cha Mulungu chinkhala bwaji mwa iye? \v 18 Bana banga okondedwa, tisakonde ndi mau cabe kapena ndililime cabe, koma mukucita ndi mchoonadi.

View File

@ -1 +1 @@
\v 19 \v 20 \v 21 \v 22 kuchokele kuli ive tiziba kuti tinachokela kuchoonadi, ndipo tisimikiza ndi mitima pamenso pake. Ngati mitima yatu itisusa koma, Mulungu nimukululu kupambana mitima yatu, Ndipo aziba zithu zonse .Wokondedwa,ngati mitima yathu sitususa,tili ndi chisimikiso kwa Mulungu.chilichonse camene tizampempa tiza landila kuchokela kwaiye, chifukwa tisunga malamulo ndipo tichita zamene zimukondwelesa iye.
\v 19 \v 20 \v 21 \v 22 Ni mwaicikuchokele kuli ive tiziba kuti tinachokela kuchoonadi, ndipo tisimikiza ndi mitima pamenso pake. Ngati mitima yatu itisusa koma, Mulungu nimukululu kupambana mitima yatu, Ndipo aziba zithu zonse .Wokondedwa,ngati mitima yathu sitususa,tili ndi chisimikiso kwa Mulungu.chilichonse camene tizampempa tiza landila kuchokela kwaiye, chifukwa tisunga malamulo ndipo tichita zamene zimukondwelesa iye.