2018-11-09 16:40:17 +00:00
|
|
|
\c 5 \v 1 Alionse wamene akhulupilila kuti Yesu anabadwa kwa Mulungu, ndiponso wamene akonda tate ndiponso akonda mwana wamene anabadwa kwaiye. \v 2 chifukwa chaichi tiziba kuti tikonda bana bamulungu: ngati takonda ndi kuchita malamulo yamulungu. \v 3 ichi ndiye chikondi chamulungu: kuti tisunge malamulo yake. ndimalamulo yake siyolema.
|