nse-x-ngoni_heb_text_reg/01/08.txt

1 line
223 B
Plaintext

\v 8 Koma ku mwana akuti, "Mpando wako, Mulungu, niwamuyaya. Ndodo ya ufumu wako ni ndodo ya cilungamo. \v 9 Wakonda cilungamo nozonda cisalungamo. Mwa ici Mulungu, Mulungu wako, wakuzoza na mafuta yacimwemwe kuposa ayako."