nya-x-nyanja_rev_text_reg/14/03.txt

1 line
452 B
Plaintext

\v 3 \v 4 \v 5 Anaimba nyimbo zasopano pamaso pa Mulungu, zamoyo zinai na akulu. Kunalibe wina opunzira nyimbo imeneyi koma chabe aja 144,000 omwe anaguliwa pa dziko la pansi. Aba nibaja bamene sanazidese na akazi, cifukwa anazisunga ku chiwelewele. Niyaba amene alondola mwana wa nkhosa kulikonse kwamene ayenda. Awa anaguliwa kuchoka pa anthu ngati ana oyamba a Mulungu ni mwana wa nkhosa. Palibe boza yamene inapezeka mkamwa mwao; niopanda chifukwa.