nya-x-nyanja_rev_text_reg/22/06.txt

1 line
273 B
Plaintext

\v 6 mungelo anakamba kwa ine, "mau aya ni yokulupilika komanso ya zoona. ambuye, mulungu wa mizimu ya aneneli, anatuma mungelo wake kuonesa akapolo ake zamene zizacitika posacedwa." \v 7 "ona! nibwera manje-manje! odala bamene bamvera mau yanga ya uneneri ya mu buku iyi."