nya-x-nyanja_rev_text_reg/21/11.txt

1 line
385 B
Plaintext

\v 11 yerusalemu anali na ulemelero wa mulungu, na kuwala kwake kunali monga mphete, monga mwala wa bafuta wa jesipa. \v 12 unali na mpanda waukulu, na polowera 12, na angelo pa khomo. pa makomo onse panalembewa maina ya mitundu 12 ya ana a israele. \v 13 ku m'mawa kunali makomo atatu, kumpoto kunali makomo atatu, ku m'mwera kunali makomo atatu komanspo kumazulo kunali makomo atatu.