nya-x-nyanja_rev_text_reg/20/07.txt

1 line
219 B
Plaintext

\v 7 pamene zaka 1000 zisila, satana azamumasula ku ndende yake. \v 8 azayenda kunamiza maiko mbali zonse za ziko lapansi-gog na magog kubaleta pamozi kuti bamenye nkhondo. bazankhala bambiri kwati ni dothi la mu manzi.