nya-x-nyanja_rev_text_reg/16/03.txt

1 line
145 B
Plaintext

\v 3 Mngelo wachiwiri anathira mbale yake mnyanja. Inasanduka magazi, monga magazi ya munthu wakufa, ndipo chilichonse cha moyo mu manzi chinafa.