nya-x-nyanja_rev_text_reg/12/01.txt

1 line
282 B
Plaintext

\c 12 \v 1 Cholangiza chikulu chinaonekela kumwamba: mukazi anavalikiwa zuba, na mwezi unali pansi pa mendo yake komanso chisote cha umfumu chinali na nyenyezi twelve pamutu pake. \v 2 Anali na pakati, komanso anali kulila na kubaba kofuna ku beleka, nakubaba kwa muzimai wa pakati.