nya-x-nyanja_rev_text_reg/09/20.txt

1 line
319 B
Plaintext

\v 20 Anthu ena onse, aja amene sanaphewe na zilango zimenezi, sanalape zoipa zamene anachita, kapena kuleka kupembeza ziwanda na mafano ya golide, siliva, bronze, minyala, na mitengo-zinthu zomwe sizipenya, kumva kapena kuyenda. \v 21 Sanalapenso pa kupha kwao, matsenga yao, chiwelewele chao kapena ncito zao za kuba.