nya-x-nyanja_rev_text_reg/09/18.txt

1 line
285 B
Plaintext

\v 18 Gawo lalikulu la anthu anafa chifukwa cha zilango zitatu zimenezi: Moto, utsi na sufule zomwe zinachoka mukamwa mwao. \v 19 Pakuti mphamvu ya akavalo inali mkamwa mwao na ku muchila kwao- chifukwa michila yao inali ngati njoka, ndipo inali na mitu yamene inali kupwetekera anthu.