nya-x-nyanja_rev_text_reg/09/16.txt

1 line
340 B
Plaintext

\v 16 Nambala ya anthu omwe anali pa msana wa akavalo ianali 200,000,000. Ninamva nambala yao. \v 17 Umu ni mwamene ninaonera akavalo mu masomphenya yanga na iwo okwerapo. Zovala pa zifuwa zao zinali zofiilira, zooneka bulumu ni zachikasu. Mitu ya akavalo imaoneka monga mitu ya nkhalamu, ndipo mkamwa mwao mumatuluka moto, utsi, na sufule.