nya-x-nyanja_rev_text_reg/07/01.txt

1 line
513 B
Plaintext

\c 7 \v 1 Pambuyo pa izi ninaona angelo anai oimilira pa makona anai a dziko, kubweza mwa mphamvu mphepo zinai za dziko kuti mphepo iliyonse isathire pa dziko la pansi, pa nyanja, kapena pa mtengo ulionse. \v 2 Ni naona mngelo wina kuchokera ku m'mawa, amene anali na chizindikiro cha Mulungu wa moyo. Analira mokweza kwa angelo anai aja omwe anapasidwa mphamvu yoononga dziko la pansi na nyanja: \v 3 "Osaononga dziko la pansi, nyanja ndi mitengo mpaka pamene tizaika zizindikiro pa mphumi pa akapolo a Mulungu."