nya-x-nyanja_rev_text_reg/06/15.txt

1 line
379 B
Plaintext

\v 15 Ndipo mamfumu na anthu olemekezeka, akulu a asilikali, olemera, amphamvu, ena onse, omasuka ni akapolo, anabisala mu mphanga na mu minyala ya m'mapiri. \v 16 Ananena kwa miyala na mapiri, "Tigweleni!" tibiseni ku nkhope ya iye amene ali pa mpando wa chimfumu ni ku mkwiyo wa mwana wa nkhosa. \v 17 Chifukwa siku la mphamvu la mkwiyo wao lafika. Ndani azakwanisa kuimilira?"