nya-x-nyanja_rev_text_reg/06/03.txt

1 line
303 B
Plaintext

\v 3 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chosindikizira cha chiwiri, ninamvera chamoyo chachiwiri kukamba ati, "bwera!" \v 4 Ndipo kavalo anatuluka osweta. Wamene anakwerapo anapasidwa mphamvu yochosa mtendere pa dziko la pansi, kuti anthu aphane okha-okha. Okwerapo ameneyu anapasidwa chimpeni chachikulu.