nya-x-nyanja_rev_text_reg/06/01.txt

1 line
307 B
Plaintext

\c 6 \v 1 Ninaona pamene mwana wa nkhosa anasegula imozi mwa zosindikizira 7, ndipo ninamva cimozi mwa zamoyo zinai zija kukamba kuti mu mau amene anamveka monga mabingu, "Bwera!" \v 2 Ninaona ndipo panali kavalo oyera. Okwerapo ananyamula uta, ndipo anapasiwa kolona. Anachoka ngati opambana kuti apambane.