nya-x-nyanja_rev_text_reg/03/05.txt

1 line
214 B
Plaintext

\v 5 Wamene apambana azapasiwa zobvala zoyera, elo sinizachosa dzina lake mu buku la moyo, ndipo nizakamba za dzina lake kwa atate, na angelo ao. \v 6 Lekani amene ali na matu amvere zamene mzimu akamba ku mipingo.