nya-x-nyanja_rev_text_reg/02/24.txt

1 line
256 B
Plaintext

\v 24 Koma kwa inu benangu baku Thyatira, aliyense amene sazasunga chipunziso ichi, ndipo sibaziba zinthu zobisika zapansi za satana- kwa inu nikamba, 'ine sinizakupasani zinango zolemesa.' \v 25 Mu njira iliyonse, mufunika kunkhala olimba mpaka nikabwere.