Thu Jan 24 2019 15:40:52 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-01-24 15:40:52 +02:00
parent f0c60309ae
commit dc197eb022
2 changed files with 1 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 10 Bamene bankala pa ziko ya pansi baza kondwela pali yeve naku sangalala. Baza pasana na mpaso chifukwa aba baneneri babili bana vutisa bantu benzo nkala pa ziko. \v 11 Koma pakapita ma siku yatatu na hafu mpepo yochoka kuli Mulungu izabangena, ndipo baza imilala pa mendo yabo. Kuyopa kukulu kuzagwera bonse bazabaona. \v 12 Ndipo bazamvela liu ikulu kuchoka ku mwamba kubauza, "Bwera pamwamba pano!" Ndipo baza yenda kumwamba mu makumbi, pamene badani babo bakali kuyanganila.
\v 10 Bamene bankala pa ziko ya pansi baza kondwela pali yeve naku sangalala. Baza pasana na mpaso chifukwa aba baneneri babili bana vutisa bantu benzo nkala pa ziko. \v 11 Koma pakapita ma siku yatatu na siku yosa kwanila mpepo yochoka kuli Mulungu izabangena, ndipo baza imilala pa mendo yabo. Kuyopa kukulu kuzagwera bonse bazabaona. \v 12 Ndipo bazamvela liu ikulu kuchoka ku mwamba kubauza, "Bwera pamwamba pano!" Ndipo baza yenda kumwamba mu makumbi, pamene badani babo bakali kuyanganila.

View File

@ -41,7 +41,6 @@
"11-03",
"11-06",
"11-08",
"11-10",
"11-13",
"11-15",
"11-16",