Wed Jan 23 2019 12:18:51 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-01-23 12:18:51 +02:00
parent 4bf5facc09
commit 7d9736129a
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 5 \v 6 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha chitatu, ninamvera chamoyo cha chitatu kukamba ati, "bwera!" ninaona kavalo wakuda, ndipo wamene anakwerapo ananyamula muyeso m'manja mwake. Ninamvera mau yamene yanamveka kwati niya chimozi mwa zamoyo kukamba ati, "muyeso wa tiligu oguliwa dinari imodzi, ndi miyeso itatu ya balele yogulidwa
\v 5 \v 6 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha chitatu, ninamvera chamoyo cha chitatu kukamba ati, "bwera!" ninaona kavalo wakuda, ndipo wamene anakwerapo ananyamula muyeso m'manja mwake. Ninamvera mau yamene yanamveka kwati niya chimozi mwa zamoyo kukamba ati, "muyeso wa tiligu oguliwa dinari imodzi, ndi miyeso itatu ya balele yogulidwa dinari imozi. Koma osaononga mafuta na vinyo."