From 3a008596c72671656626c5fe86fc5c4d7b0cb7d9 Mon Sep 17 00:00:00 2001 From: tsDesktop Date: Tue, 22 Jan 2019 20:03:46 +0200 Subject: [PATCH] Tue Jan 22 2019 20:03:46 GMT+0200 (South Africa Standard Time) --- 01/01.txt | 2 +- 1 file changed, 1 insertion(+), 1 deletion(-) diff --git a/01/01.txt b/01/01.txt index cee5aaa..29d40e9 100644 --- a/01/01.txt +++ b/01/01.txt @@ -1 +1 @@ -\c 1 \v 1 \v 2 \v 3 Ili ni vumbuluso la Yesu Kristu lamene Mulungu anamupasa kuti aonese akapolo ake zamene zizacitika manje-manje. Anazionesa kupitira mwa mngelo wake kwa Yohane. Yohane anacitira umboni mau a Mulungu na pa umboni operekedwa wa Yesu Khristu, zinthu zonse zamene anaona. Ni odala amene abelenga mokweza \ No newline at end of file +\c 1 \v 1 \v 2 \v 3 Ili ni vumbuluso la Yesu Kristu lamene Mulungu anamupasa kuti aonese akapolo ake zamene zizacitika manje-manje. Anazionesa kupitira mwa mngelo wake kwa Yohane. Yohane anacitira umboni mau a Mulungu na pa umboni operekedwa wa Yesu Khristu, zinthu zonse zamene anaona. Ni odala amene abelenga mokweza, na amene amvera mau ya uneneri, na bamene bagonjera zamene zinalembedwamo, cifukwa nthawi ili pafupi. \ No newline at end of file