\v 13 \v 14 \v 15 Mngelo wa namba 6 analiza lipenga lake, ndipo ninamva mau ochokera mu nyanga ya pa guwa la golide yomwe ipezeka kwa Mulungu. Liu linanena na mngelo wa nambala 6 yemwe anali na lipenga, "masula angelo anai omwe niomangiwa pa msinje waukulu wa Euphrates." Angelo anai omwe anakonzedwera nthawi imenei, siku limeneli, mwezi umeneo,