Thu Jul 15 2021 22:24:33 GMT+0100 (British Summer Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-07-15 22:24:33 +01:00
parent 7da9c9b201
commit fb70c15482
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 3 \v 4 \v 5 ndipo mungeli wamene tina kambisana naye ana chokapo ndiponso mungeli winango anachoka panja kuyendo kumana na eve. 4mungeli wa chibili anakamba kuli eve, '' tamanga ndipokukamba kuli munyamata uja; kamba, 'yelusalema azankala ziko yoseguka chifukwa chakupaka kwa bantu na vibeto mukati mwake. 5pakuti ine-uku nikukamba kwa YEHOVA-nizankala kuli eve chipupa cha mulilo cho muchingiliza, ndiponso nizankala ulemelelo pakati pake.
\v 3 \v 4 \v 5 ndipo mungeli wamene tina kambisana naye ana chokapo ndiponso mungeli winango anachoka panja kuyendo kumana na eve. 4mungeli wa chibili anakamba kuli eve, '' tamanga ndiponso ukambe kuli munyamata uja; kuti, 'yelusalema azankala ziko yoseguka chifukwa chakupaka kwa bantu na vibeto mukati mwake. 5pakuti ine-uku nikukamba kwa YEHOVA-nizankala kuli eve chipupa cha mulilo cho muchingiliza, ndiponso nizankala ulemelelo pakati pake.