nya-x-nyanja_sng_text_reg/01/12.txt

1 line
276 B
Plaintext

\v 12 Mfumu ili chigonere pabedi pake, nade wanga anali kutulutsa kununkhira kwake. \v 13 Wokondedwa wanga ali ngati thumba la mule limene limagona pakati pa mabere anga usiku wonse. \v 14 Wokondedwa wanga ali kwa ine ngati tsango la maluwa a heni m'minda yamphesa ya En-Gedi.