nya-x-nyanja_sng_text_reg/01/09.txt

1 line
253 B
Plaintext

\v 9 Wokondedwa wanga, ndakufanizitsa ndi mwana wamkazi wa mahatchi a Farao. \v 10 Masaya ako ndi abwino ndi zokongoletsera, khosi lako ndi zokongoletsa za zingwe. \v 11 Tikupangira zokongoletsera zagolide ndi zomangira zasiliva. Mkazi akuyankhula yekha