nya-x-nyanja_sng_text_reg/05/15.txt

1 line
155 B
Plaintext

\v 15 Mendo yake ili ngati sadamila ya mwala obekelela, zoikwa pazisulo zagolide obekelela; Maonekedwe yake yali monga Lebanoni, yabwino ngati mikungudza.